Lero kunja kwa chaso Mutu ukupwetekaso Zoyenda mutu mwanga nzochitisa kaso Kuyesa kuthamanga haso Koma sizikuthekaso Aaaaaaa Oyee (Chorus) Koma ndikudziwa yemwe angandithandize Za mavuto anga yemwe angandimvesese Ndi Yehova Yekha yemwe analenga zonse Ndipo ndiye yekha yemwe akudziwa zonse Mundipase mphamvu Aaaaaaaa Ndikhale waukali ngati mavu Mavuto akabwera ndiziwaluma ndikutaya